Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Zifukwa Zokhalila ndi Cikhulupililo—Cikondi Cimagonjetsa Kupanda Cilungamo

Zifukwa Zokhalila ndi Cikhulupililo—Cikondi Cimagonjetsa Kupanda Cilungamo

Alwande ndi Emma afotokoza mmene malonjezo a m’Baibulo anawalimbikitsila kugwilitsa nchito cikondi pothandiza anthu m’njila yabwino koposa. Panthawi imodzimodzi iwo akukhala mogwilizana ndi anthu ena palipano.