Nehemiya: “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”

Nehemiya anatsogolela nchito yomanganso mpanda wa Yerusalemu komanso kubwezeletsa kulambila koona.

Nehemiya: “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”—Gawo 1

Nehemiya anamanganso mpanda wa Yesrusalemu olo kuti anali kukumana na zitsutso zosiyana-siyana.

Nehemiya: “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”—Gawo 2

Nehemiya anatsiliza kumanganso mpanda, koma kodi iye adzakwanitsa kuthandiza Aisiraeli kuti ayambenso kulambila koona?