Nehemiya: “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”—Gawo 1
Nehemiya anasiya udindo wake m’Nyumba ya Mfumu ku Susani kuti akamangenso mpanda wa mzinda waukulu wa Yehova. Komabe, iye anakumana na ziyeso zambili pogwila nchito imeneyi. Kodi pemphelo na kulimba mtima zinam’thandiza kuti atsilize nchitoyi?