‘Ndithu Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye ndi Kristu’

Pakapita nthawi, mungayambe kukayikila ndipo cikhulupililo cingafooke. Limbitsani cikhulupililo canu mwa Yesu, Mesiya wolonjezedwa ndi Mfumu ya Ufumu wa Mulungu.

‘Ndithu Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye ndi Kristu’ (Mbali 1)

N’ciani cimakucititsani kutsimikizila kuti Mulungu anaika Yesu kukhala Ambuye ndi Kristu?

‘Ndithu Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye ndi Kristu’ (Mbali II)

Onani zimene zingakuthandizeni kukhala ndi cikhulupililo colimba mwa Yesu.