Onani zimene zilipo

Mfundo Zothandiza Mabanja

Pagawo limeneli pali nkhani zosiyanasiyana zokhala na malangizo ocokela m’Baibo othandiza mabanja. a Kuti muone m’ndandanda wa nkhani zosiyanasiyana zothandiza mabanja, pitani pagawo lakuti Anthu Okwatilana Komanso Mabanja.

a Maina a anthu ena omwe achulidwa m’nkhanizi asinthidwa.

Raising Children

Kuphunzitsa Mwana Wanu Nkhani Zokhudza Kugonana

Masiku ano ana akumaona ndiponso kumva zinthu zokhudza kugonana ali aang’ono kwambili. Kodi muyenela kudziŵa zotani? Kodi mungacite ciyni kuti muziteteza ana anu?