Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NYIMBO 155

Cimwemwe Cathu Camuyaya

Cimwemwe Cathu Camuyaya

(Salimo 16:11)

  1. 1. Kumwamba kuli nyenyezi

    ndipo ziwala.

    Munakongoletsa usana

    na usiku.

    Manja anu anapanga

    zinthu zonse mukondwela

    Mukaziona.

    (KOLASI)

    Cilengedwe canu M’lungu

    Na uthenga wa Ufumu

    Zimatikondweletsa.

    Cikondi canu cosatha

    Ndiye cuma camuyaya.

    Ndimwe cimwemwe cathu.

    Inde, ca muyaya.

  2. 2. Yehova tili na zonse

    zosangalatsa—

    Zonse tiona na maso,

    zikhudza mtima.

    Mwatipatsa umuyaya

    Mumitima yathu,

    Na cimwemwe cosatha.

    (KOLASI)

    Cilengedwe canu M’lungu

    Na uthenga wa Ufumu

    Zimatikondweletsa.

    Cikondi canu cosatha

    Ndiye cuma camuyaya.

    Ndimwe cimwemwe cathu.

    Inde, ca muyaya.

    (BILIJI)

    Munapeleka Yesu

    Kuti atifele

    Sitikanapeza cimwemwe

    Popanda nsembe yake.

    (KOLASI)

    Cilengedwe canu M’lungu

    Na uthenga wa Ufumu,

    Zimatikondweletsa.

    Cikondi canu cosatha

    Ndiye cuma camuyaya.

    Ndimwe cimwemwe cathu

    Inde, ca muyaya.

    (KOLASI)

    Cilengedwe canu M’lungu

    Na uthenga wa Ufumu

    Zimatikondweletsa

    Cikondi canu cosatha

    Ndiye cuma camuyaya

    Ndimwe cimwemwe cathu

    Inde, ca muyaya.

(Onaninso Sal. 37:4; 1 Akor. 15:28.)