Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NYIMBO 157

Mtendele Wosatha Pamapeto Pake!

Mtendele Wosatha Pamapeto Pake!

(Salimo 29:11)

  1. 1. M’dziko lamavuto

    Anthu a M’lungu

    Akukhala pamtendele.

    Ndipo tidziŵa

    kuti mavutowa

    Adzathadi

    posacedwa.

    (KOLASI)

    Pamapeto pake

    tidzauona

    Mtendele wosatha.

    Pa dziko lapansi

    na kumwambako,

    Konse kudzakhala

    Mtendele.

  2. 2. M’dziko la tsopano

    anthu onse

    Adzakhaladi amodzi.

    Ulamulilo

    tidzauonewo

    Udzakhala wacikondi.

    (KOLASI)

    Pamapeto pake

    tidzauona

    Mtendele wosatha.

    Pa dziko lapansi

    na kumwambako,

    Konse kudzakhala

    Mtendele.

    (KOLASI)

    Pamapeto pake

    tidzauona

    Mtendele wosatha.

    Pa dziko lapansi

    na kumwambako,

    Konse kudzakhala.

    (KOLASI)

    Pamapeto pake

    tidzauona

    Mtendele wosatha.

    Pa dziko lapansi

    na kumwambako,

    Konse kudzakhala

    Mtendele,

    Mtendele!

(Onaninso Sal. 72:1-7; Yes. 2:4; Aro. 16:20)