Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mphamvu Yoposa Yanga

Mphamvu Yoposa Yanga

Daunilodi:

  1. 1. Nthawi zonse maganizo

    Osautsa akaculuka,

    Nimapemphela podziwa kuti

    Yehova

    Anithandiza.

    (MWANA WA KOLASI)

    Nipempha

    Munipatse mzimu wanu.

    (KOLASI)

    Mwa mzimu wanu

    Ningathe kuuluka inde m’mwamba.

    Monga ciwombankhanga couluka,

    Sin’dzafoka, nidzalimba.

    Mwa mzimu wanu M’lungu.

  2. 2. Citonthozo canu M’lungu

    Canipatsa mphamvu kuti nithe

    Kuthandiza ena kuona

    Cikondi canu cosasintha.

    (MWANA WA KOLASI)

    Nipempha

    Munipatse mzimu wanu.

    (KOLASI)

    Mwa mzimu wanu

    Ningathe kuuluka inde m’mwamba.

    Monga ciwombankhanga couluka,

    Sin’dzafoka, nidzalimba.

    Mwa mzimu wanu M’lungu.

    (KOLASI)

    Mwa mzimu wanu

    Ningathe kuuluka inde m’mwamba.

    Monga ciwombankhanga couluka,

    Sin’dzafoka, nidzalimba.

    Mwa mzimu wanu M’lungu,

    Mwa mzimu wanu M’lungu,

    Mwa mzimu wanu M’lungu.