Cikondi ca Paubale
Daunilodi:
1. Konse mungapite mupeza banja
Ndipo konse mudzapeza anthu a Yehova
Mudzapeza cikondi ca paubale
Tikondana oh.
2. Abale na alongo mu dziko
Amatengela Yehova na Yesu
Mu cikondi
Iwo ni banja la cikondi
Tikondana
(KOLASI)
Yehova amatisunga
Akonda onse
3. M’kati mwatengo na mumaphili
Mu matauni akulu na kumidzi
Mudziŵe namwe ndimwe anthu a M’lungu
Tikondana oh.
(KOLASI)
Yehova amatisunga
Atikonda tonse.
(BILIJI)
Mudzikoli nimovuta
Zoonadi nimoopsa
N’zosangalatsadi kudziŵa
Yehova na anthu ake
4. Yesu anaphunzitsa cikondi
Kuti anthu azitengela cikondi
ca Yehova, namwe muli pakati pawo
Tikondana
Tikondana oh.