Cimwemwe ca Misonkhano Ikulu
Daunilodi:
1. Nyimbo zamalimba zisanayambe,
Tili pamodzi, tili pamodzi.
Mudzikoli muli m’sokhonezo
Komabe ise tigwilizana.
(KOLASI)
Ndise’a bale ndise’a longo ana na makolo.
Nikukonda ngakhale sitinaonanepo.
Ndise’a bale ndise’a longo ana na makolo.
Nikukonda ngakhale sitinaonanepo.
2. Onani anthu ngati nyanja ambilimbili,
Niona anthu amene sinidziŵa,
Koma sivuto ndise banja.
Anipatsa moni mwacimwemwe,
Akusekelela.
Nikumva mphumulo ngati mwana,
Nifuno lila nigwileni.
(KOLASI)
Ndise’a bale ndise’a longo ana na makolo.
Nikukonda ngakhale sitinaonanepo.
Ndise’a bale ndise’a longo ana na makolo.
Nikukonda ngakhale sitinaonanepo.
(BILIJI)
Capamodzi
Timenya nkhondo,
Nithandize
kuupeza moyo wosathawo.
(KOLASI)
Ndise’a bale ndise’a longo ana na makolo.
Nikukonda ngakhale sitinaonanepo.
Ndise’a bale ndise’a longo ana na makolo.
Nikukonda ngakhale sitinaonanepo.
Nikukonda ngakhale sitinaonanepo.