Dekhani ndipo Pemphelani
Daunilodi:
1. Moyo ungakhale wovuta
Ukakumana na mavuto ambili.
Mabwenzi angakuvutitseni
Pemphelani kwa M’lungu—
Kwa Yehova.
(KOLASI)
Limbani; Musagwe
Yehova m’dalileni.
’fikeni m’pemphelo
Mudzapambanadi.
Ngakhale zivute,
Yehova, adzathandiza
M’sakaikile, iyai;
Imwe mupempheni.
M’sangalatseni
Mudzapambana.
2. Timavutika nthawi zina.
Tilibe ndalama zogulila zinthu.
Komabe timasangalaladi,
Kugaŵilako ena—
Zinthu zathu.
(KOLASI)
M’sayope; Limbani.
Yehova m’dalileni.
M’fikeni m’pemphelo
Mudzapambanadi.
M’kafo’ka, Limbani.
Yehova adzathandiza.
Ali na imwe, Limbani
Imwe mupempheni.
M’sangalatseni.
Mudzapambana.
(KOLASI)
Yehova m’dalileni.
M’fikeni m’pemphelo
Mudzapambanadi.
M’kafo’ka, Limbani.
Yehova adzathandiza.
Ali na imwe, Limbani.
Imwe mupempheni.
M’sangalatseni.
Mutamandeni.