“Kondwelani Nthawi Zonse”
Daunilodi:
1.Ona m’mwamba, mwabwino.
Kuwala kwa dzuŵa.
M’lungu watipatsa madalitso oculuka,
Koma mphatso yake yoposa zonse n’cikondi cake.
(KOLASI)
Ti’mbile Yehova mokondwa.
Nakum’tumikila—
Tikatelo tidzapezadi,
Cimwemwe cosatha.
Kondwelani! nthawi zonse!
Kondwelani! nthawi zonse!
2.Pamodzi, ndife banja—
Umodzi ni wabwino—
Zonsezi ni mphatso zocokela kwa Yehova.
Timakondwelabe ngakhale kuti titsutsidwa.
(KOLASI)
Ti’mbile Yehova mokondwa.
Nakum’tumikila—
Tikatelo tidzapezadi,
Cimwemwe cosatha.
Kondwelani! nthawi zonse!
Kondwelani! nthawi zonse!
(BILIJI)
M’lungu adzatipatsa dziko latsopano.
Imfa ya Yesu Khristu yatimasula.
(KOLASI)
Ti’mbile Yehova mokondwa.
Nakum’tumikila—
Tikatelo tidzapezadi,
Cimwemwe cosatha.
Kondwelani! nthawi zonse!
Kondwelani! nthawi zonse!
Kondwelani! nthawi zonse!
Kondwelani! nthawi zonse!
Kondwelani! nthawi zonse!
Kondwelani! nthawi zonse!
Nthawi zonse!