Kucita Zoyenela
Daunilodi:
1. Aliyense amadziŵa
Munthu angakhale m’nzake.
Nimadziŵa zoyenela
Nimadziŵanso zoipa.
Nikondwela kupezanso
Anzanga onilimbitsa.
Anzangawa ni abwino
Anifunila zabwino.
(KOLASI)
Mu mtima mwanga nimadziŵadi,
Yehova ndimwe munithandiza
Kucita zoyenela.
2. Mtima wanga
Umadziŵa zinthu zoniyenelela.
Kuŵelenga mu baibo
Kumanilimbikitsadi.
Nadziŵadi, na kuona
Kumene kuli mabwenzi
Oyenela ndi abwino.
Aŵa ni mphatso kwa ine.
(KOLASI)
Mu mtima mwanga nimadziŵadi
Yehova ndimwe munithandiza
Kuchita zoyenela.