Mabwenzi Azoona
Daunilodi:
1. Moyo ungakhaledi ovuta m’dziko loipali.
Tifunikila mabwenzi angatilimbikitse
Komabe ise tingacite bwanji popeza mabwenzi?
Tikumbukile mawu a M’lungu.
(KOLASI)
M’nzako
Amakukonda
Samakusiya
Ali nawe pamavuto
Samakunama
Amayamikila
Athandiza kuyenda m’njila
Yakumoyo ndipo akonda M’lungu
Ndiyedi m’nzako.
2. Mabwenzi amatikonda, ndipo timadziŵa
Conco pamavuto tisafooke tipemphe kwa M’lungu
Acikulile na acicepele tonse tizikondana
Tidzapeza moyo wamuyaya.
(KOLASI)
M’nzako
Amakukonda
Samakusiya
Ali nawe pamavuto
Samakunama
Amayamikila
Athandiza kuyenda m’njila
Ya kumoyo ndipo akonda M’lungu
Ndiyedi m’nzako.
(BILIJI)
Wokukonda
Ofuna kuti utumikile M’lungu
Ni wodalilika amakamba za zoona
Ndiyedi m’nzako.
(KOLASI)
M’nzako
amakukonda
Samakusiya
Ali nawe pamavuto
Samakunama
Amayamikila
Athandiza kuyenda m’njila
Yakumoyo ndipo akonda M’lungu
(KOLASI)
M’nzako
Amakukonda
Samakusiya
Ali nawe pamavuto
Samakunama
Amayamikila
Athandiza kuyenda m’njila
Yakumoyo ndipo akonda
M’lungu ndiyedi m’nzako.
Ndiyedi m’nzako ooh.
Ndiyedi m’nzako.