“Menya Nkhondo Yabwino Ya Cikhulupililo”
Daunilodi:
1. Nthawi zina zimavuta.
Nimamvela monga nzelu zasila.
Nimasoŵa na cocita.
Nimagwetsa cabe misozi.
(MWANA WA KOLASI)
Koma M’lungu ali nane
Nidziŵa kuti nikavutika mawu ake M’lungu.
amanitonthoza kuti:
(KOLASI)
Kwatsaladi pang’ono,
Nizapukuta misozi.
Kwatsaladi pang’ono
dziko idzasintha.
Iwe limbikila
Nidzakuthandiza.
N’dzakuthandiza.
2. Mawu ake amalimbitsa
Amanithandidza pa mavuto.
(MWANA WA KOLASI)
Koma M’lungu ali nane
Nidziwa kuti nikavutika mawu ake M’lungu
amanitonthoza kuti:
(KOLASI)
Kwatsaladi pang’ono
Nizapukuta misozi.
Kwatsaladi pang’ono
dziko idzasintha
Iwe limbikila
Nidzakuthandiza.
N’dzakuthandiza
Nidzakuthandiza
Nidzakuthandiza.
(BILIJI)
N’dzakuthandiza
N’dzakuthandiza
N’dzakuthandiza.
(KOLASI)
Kwatsaladi pang’ono
Nizapukuta misozi.
Kwatsaladi pang’ono
dziko idzasintha
Iwe limbikila
Nidzakuthandiza.