Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Nikupatsani Zonse Nili Nazo

Nikupatsani Zonse Nili Nazo

Daunilodi:

  1. 1. Yehova nikupatsani zonse nili nazo.

    Nifuna mukondwele na zocita zanga zonse.

    Nithandizenso ena kumvela mawu anu.

    Kulalikila kumanipatsadi cimwemwe.

    (MWANA WA KOLASI)

    Kutumikila imwe Yehova kunilimbitsa

    Nidzayendabe m’njila zanu Mulungu wanga.

    (KOLASI)

    Yehova M’lungu nikutamandani.

    Moyo wanga nipeleka kwa imwe

    Nikupatsani zonse nili nazo.

    Nidzakutumikilani na mtima wonse.

  2. 2. Nidzaonetsadi cikondi kwa abale.

    Modzipeleka nifuna kuthandiza ena

    Kupatsa ena kumabweletsadi cimwemwe

    Nimakondwela poŵathandiza ovutika.

    (MWANA WA KOLASI)

    Kutumikila imwe Yehova kunilimbitsa

    Nidzayendabe m’njila zanu Mulungu wanga.

    (KOLASI)

    Yehova M’lungu nikutamandani.

    Moyo wanga nipeleka kwa imwe

    Nikupatsani zonse nili nazo.

    Nidzakutumikilani na mtima wonse.

    (KOLASI)

    Yehova M’lungu nikutamandani.

    Moyo wanga nipeleka kwa imwe

    Nikupatsani zonse nili nazo.

    Nidzakutumikilani na mtima wonse.