Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tithamange pa Mpikisano

Tithamange pa Mpikisano

Daunilodi:

  1. 1. Yang’ana za kutsogolo.

    Yang’ana pa mphoto

    Usaceuke.

    Ino ndiyo nthawi

    Yolimba mtima.

    Usalole za m’dziko

    Kukufo’ketsa.

    (KOLASI)

    Tiye thamanga!

    Thamanga!

    Mpaka ukapeze moyo.

    Tiye thamanga!

    Usaceuke.

    Tiye thamanga!

    Thamanga!

    Usaime, limbikilabe.

    Pitabe patsogolo.

    Tiye thamanga.

  2. 2. Mphoto yathu,

    Inde, niyamuyaya.

    Tidzadalitsidwa

    Posacedwapa.

    (KOLASI)

    Tiye thamanga!

    Thamanga!

    Mpaka ukapeze moyo.

    Tiye thamanga!

    Usaceuke.

    Tiye thamanga!

    Thamanga!

    Usaime, limbikilabe.

    Pitabe patsogolo.

    Tiye thamanga.

    Udzapambana.

    (BILIJI)

    Dziko lifuna

    Tiziceuka,

    Kuti tisapambane.

    Iwe khala wolimba.

    Tiye thamanga!

    Thamanga!

    Thamanga!

    Thamanga!

    (KOLASI)

    Tiye thamanga!

    Thamanga!

    Mpaka ukapeze moyo.

    Tiye thamanga!

    Usaceuke,

    Tiye thamanga!

    Thamanga!

    Usaime, limbikilabe.

    Pitabe patsogolo.

    Tiye thamanga.

    Udzapambana!

    Udzapambana! (udzapambana)

    Tiye tithamangebe.

    Tiye usafoke

    Thamanga! (oo! Usafo’ke)

    Tithamange pamodzi.

    Tidzapambana.