Tiyamikila
Daunilodi:
1. Nikavutika
Mumaganizo
Mumamvela
Niyamikila.
2. Tikavutika
Mutithandiza
Mumayankha
Tiyamikila.
3. Tisadele nkhawa
Za ciliconse
Mudzatithandiza.
Ngati tipitiliza kudalila
Inu nthawi zonse.
4. Pa zinthu zonse
Muthandiza
Tiyamikila.
5. Mumakonda okukondani
M’zinthu zonse tiyamikila.