Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tiyenibe

Tiyenibe

Daunilodi:

  1. 1.Timafuna—

    Timakonda

    Kumutumikila

    M’lungu wathu.

    Sitifuna

    Kuti mwayi,

    Wotumikilawu

    Utipite

    (KOLASI)

    Tiyenibe!

    Tisayope.

    Tisakaikile;

    Tiutenge

    Utumiki.

    Tim’dalile Yehova.

    Tiyenibe

    Mwacimwemwe.

  2. 2.Mlungu wathu;

    Adziŵadi

    Zonse mtima

    wathu umafuna.

    Olo kuti

    Zingavute

    Tim’dalile iye

    Nthawi zonse.

    (KOLASI)

    Tiyenibe!

    Tisayope.

    Tisakaikile;

    Tiutenge

    Utumiki.

    Tim’dalile Yehova.

    Tiyenibe

    Mwacimwemwe.

  3. 3.Tisayope

    Utumiki

    Wa nthawi zonsewu.

    Tisayope.

    Tidzapeza

    Madalitso ambili

    Na cimwemwe

    Camuyaya.

    (KOLASI)

    Tiyenibe!

    Tisayope.

    Tisakaikile;

    Tiutenge

    Utumiki.

    Tim’dalile Yehova.

    Tiyenibe

    Mwacimwemwe.

    Tiyenibe!

    Tisayope.

    Tisakaikile;

    Tiutenge

    Utumiki.

    Tim’dalile Yehova.

    Tiyenibe

    Mwacimwemwe

    Tiyenibe.