Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.
Benin
ARTJB (Association religieuse des Témoins de Jéhovah du Bénin)
Route Inter-Etat Cotonou-Parakou
AB-CALAVI
BENIN
+229 97-97-00-60
+229 21-36-01-14
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:00hrs mpaka 10:45hrs ndi 13:00hrs mpaka 13:45hrs
Nthawi yoona malo: Mphindi 45
Zimene Timacita
Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’cinenelo ca Cibariba, Cifoni, Ciguni, Cijula, Cikabiye, Cimoore, ndi Cizarima. Ndiponso timatumiza mabuku ku mipingo yoposa 500 ndi tumagulu m’dziko lathu, ku Burkina Faso, ku Niger, ndi ku Togo.