Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Brazil

Rodovia SP-141 - km 43

CESÁRIO LANGE-SP

18285-901

BRAZIL

+55 15-3322-9000

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 10:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 15:00hrs

Nthawi yoona malo: Ola limodzi ndi mphindi 40

Zimene Timacita

Timasindikiza Mabaibulo 36 milliyoni, mabuku ndi tumabuku ndipo timatumiza mabuku olema matani pafupifupi 7,000 a zinenelo zoposa 90 mwezi uliwonse.

Tengani kapepala koonetsa malo.