Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.
Central African Republic
58 rue du Stade Boganda
BANGUI
CENTRAL AFRICAN REPUBLIC
+236 21-61-20-70
+236 21-61-89-25
+236 70-11-08-00
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:00hrs mpaka 11:00hrs
Nthawi yoona malo: Ola limodzi
Zimene Timacita
Timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova yophunzitsa anthu Baibulo ndi yomanga Nyumba za Ufumu m’dzikoli ndi la Chad. Ndiponso timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’cinenelo ca Cisango ndi zinenelo zina 7.