Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Côte d’Ivoire

Rue J-58 - Lot 1758

Deux-Plateaux

3ème tranche, Vallon

ABIDJAN

CÔTE D’IVOIRE

+225 2241-3606

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

14:00hrs mpaka 16:00hrs

Nthawi yoona malo: Ola limodzi

Zimene Timacita

Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’Ciabeyi, Ciatiyi, Cibole, Cibete, Cigulo, Cigwele Cisenufo ndi Ciyakoba. Ndiponso timaika pa ma CD tumabuku ndi maseŵelo omvetsela m’zinenelo zambili.

Tengani kapepala koonetsa malo.