Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Dominican Republic

Autopista San Isidro #100

(Al lado de Coral Mall, Frente a Savica)

SANTO DOMINGO ESTE

DOMINICAN REPUBLIC

+1 809-595-4007

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.

Nthawi yoona malo: Ola limodzi

Zimene Timacita

Timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova yophunzitsa anthu Baibulo m’dziko lathu. Poona malo mudzaonanso zinthu zina zokhudza mbili ya Mboni za Yehova.

Tengani kapepala koonetsa malo.