Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.
Ecuador
Sociedad de Estudiantes de la Biblia - Testigos de Jehová
Kilometer 23,5 via a la Costa (600 meters before the tollbooth)
GUAYAQUIL
ECUADOR
+593 4-273-8015
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:30hrs mpaka 10:30hrs ndi 13:30hrs mpaka 15:30hrs.
Nthawi yoona malo: Ola limodzi ndi hafu
Zimene Timacita
Timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova m’mipingo yoposa 900. Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’Cikwicuwa, m’Cishuwa ndi m’cinenelo ca manja ca ku Ecuador.