Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Kenya

Elgeyo Marakwet Rd

Kilimani area near Adams Arcade

NAIROBI

KENYA

+254 20-387-3211

+254 20-387-3212

+254 20-387-3213

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.

Nthawi yoona malo: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timacita

Timayang’anila nchito yomasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’zinenelo 10 kuphatikizapo cinenelo ca manja ca ku Kenya. Timapanga ma CD a zofalitsa ndi mavidiyo a zinenelo za m’dzikoli. Timathandizanso nchito ya Mboni za Yehova m’maiko angapo oyandikana ndi dzikoli.

Tengani kapepala koonetsa malo.