Onani zimene zilipo

Lipoti la Msonkhano wa maiko

Lipoti la Msonkhano wa maiko

Pa misonkhano ya maiko, anthu a m’maiko ambili, a zinenelo zosiyanasiyana, ndiponso a mitundu yosiyanasiyana, amasangalala kwambili ndi maphunzilo a m’Baibulo ndiponso kuceza ndi Akristu anzao kwa masiku angapo.