Onani zimene zilipo

Tikuitanilani ku Msonkhano Wacigawo wa Mboni za Yehova wa 2023 wa Mutu Wakuti “Khalani Oleza Mtima”!

Tikuitanilani ku Msonkhano Wacigawo wa Mboni za Yehova wa 2023 wa Mutu Wakuti “Khalani Oleza Mtima”!

Koposa kale lonse, masiku ano tifunika kukhala oleza mtima. Koma kodi kukhala woleza mtima kumatanthauza ciyani kwenikweni? Ndipo kungakhudze bwanji umoyo wathu wa tsiku na tsiku? Dzamveni mayankho pa msonkhano wacigawo wa 2023 wa mutu wakuti “Khalani Oleza Mtima”!