Nyuzi
Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila mu 2022
Wa m’Bungwe Lolamulila akutilimbikitsa kukhala okonzeka kusintha galeta la Yehova likamayenda.
Ciunikilo Na. 6 ca Bungwe Lolamulila mu 2022
Wa m’Bungwe Lolamulila akupeleka lipoti la zocitika zosangalatsa zaposacedwa komanso kulengeza lemba la caka ca 2023.
Ciunikilo Na. 5 ca Bungwe Lolamulila mu 2022
Wa m’Bungwe Lolamulila akufotokoza zimene zinathandiza abale athu kupilila cizunzo mu ulamulilo wakale wa Soviet Union, ndipo akutitsimikizila kuti Yehova adzatithandiza nthawi zonse.
Ciunikilo Na. 4 ca Bungwe Lolamulila mu 2022
Wa m’Bungwe Lolamulila akutilimbikitsa kupilila mayeso mokhulupilika komanso mwacimwemwe potengela citsanzo ca abale athu a kum’mawa kwa Europe.
Ciunikilo Na. 3 ca Bungwe Lolamulila mu 2022
Wa m’Bungwe lolamulila akufotokoza mfundo zimene zingatithandize kucepetsako nkhawa zimene tingakhale nazo tikaganizila za nkhondo imene ikucitika kum’mawa kwa Europe.
Ciunikilo Na. 2 ca Bungwe Lolamulila mu 2022
M’bale wa m’Bungwe Lolamulila akufotokoza mmene abale na alongo athu akhalilabe okhulupilika pamene akukumana na mayeso.
2020—Ciunikilo Na. 9 ca Bungwe Lolamulila
M’bale wa m’Bungwe Lolamulila afotokoza kufunika kopitilizabe kukhala chelu na mmene tingadzitetezele ife tokha na anthu ena ku matenda a COVID-19.
2020—Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila
M’bale wa m’Bungwe Lolamulila afotokoza mmene maulosi a m’Baibo angatithandizile kupilila pa nthawi ya mliliwu.
2020—Ciunikilo Na. 7 ca Bungwe Lolamulila
M’bale wa m’Bungwe Lolamulila afotokoza zimene zingathandize acicepele kupilila mavuto obwela cifukwa ca mliliwu.
Ciunikilo Na. 6 ca Bungwe Lolamulila mu 2020
Wa m’Bungwe Lolamulila afotokoza mmene cakudya cauzimu capitilizila kupelekedwa mosasamala kanthu za mlili.
Mlandu wa Mboni za Yehova Uloŵanso mu Khoti ku Taganrog —Kodi Cilungamo Cidzacitika Liti?
Kodi Mboni 16 zamtendele ku Russia zidzamangidwa cifukwa ca cikhulupililo cawo?