Onani zimene zilipo

Acinyamata Komanso Acinyamata Acikulilepo

Malangizo a m’Baibo angakuthandizeni kuthana na zovuta komanso kukulitsa maluso ofunika. a

a Mayina a anthu ena ochulidwa m’nkhanizi asinthidwa.

Zimene Acinyamata Anzanu Amakamba

Mwina mukukumana na mavuto omwe n’kuyamba kukumanapo nawo. Onani zimene anzanu amacita pothana na mavutowo.

Tukadoli Tojambula Pamanja

Kodi mumakumanako na zovuta zimene mumaona kuti n’zosatheka kuthana nazo? Ngati n’conco, tumavidiyo utu tudzakuthandizani kudziŵa mmene mungacitile nawo mavuto amene acinyamata ambili amakumana nawo.

Mayankho pa Mafunso 10 Amene Acicepele Amafunsa

Peza malangizo amene angakuthandize kukhala na umoyo wabwino.