Onani zimene zilipo

TUKADOLI TOJAMBULA PAMANJA

N’cifukwa Ciyani Muyenela Kukhala Woona Mtima?

N’cifukwa Ciyani Muyenela Kukhala Woona Mtima?

Mukayamba kukamba mabodza, cingakhale covuta kuti muleke khalidwelo. Onani zotulukapo za kukhala wosaona mtima, komanso mmene timapindulila tikamacita zinthu moona mtima.