Onani zimene zilipo

Zimene Acinyamata Anzanu Amakamba

Onelelani mavidiyo a acinyamata a m’mayiko osiyanasiyana akufotokoza mavuto amene amakumana nawo komanso zimene amacita pothana na mavutowo.

 

Zimene Acicepele Anzanu Amakamba Zokhudza Mafoni

Kwa acicepele ambili, foni ni yofunika ngako. Ubwino na kuipa kwa mafoni.

Zimene Acinyamata Amakamba Zokhuza Kuzengeleza

Onani zimene acinyamata amakamba zomwe zingapangitse munthu kuzengeleza komanso onani mapindu oseŵenzetsa nthawi yanu mwanzelu.

Zimene Acinyamata Amakamba Zokhuza Maonekedwe

N’cifukwa ciyani zimakhala zovuta kwa acinyamata kukhala na maganizo oyenela pa maonekedwe awo? N’ciyani cingaŵathandize?

Acinyamata Akamba za Kukhulupilila mwa Mulungu

Mu vidiyo iyi ya mphindi zitatu, acinyamata afotokoza zimene zinaŵathandiza kukhulupilila kuti Mlengi aliko.

Acinyamata Akamba za Kuŵelenga Baibo

Kuŵelenga si kopepuka, koma kuŵelenga Baibo kumapindulitsa. Acinyamata anayi afotokoza mmene anapindulila poŵelenga Baibo.

Zifukwa Zokhalila na Cikhulupililo—Niziyendela Mfundo za Mulungu Kapena Zanga

Acinyamata akufotokoza mmene anapewela makhalidwe oipa a anzawo ku sukulu.

Umoyo Wabwino Koposa

Kodi mufuna umoyo waphindu? Mvetselani pamene Cameron afotokoza mmene anapezela umoyo wokhutilitsa m’njila yosayembekezeleka.