B14-A
Mipimo ya vinthu na malonda
-
Mipimo ya vinthu vamadzi
-
Kori (Mitsuko 10 / Mahini 60)
Malitro 220 / Magaloni 58,1
-
Mtsuko (Mahini 6)
Malitro 22 / Magaloni 5,81
-
Hini (Malogi 12)
Malitro 3,67 / Mapainti 7,75
-
Logi (1 ⁄ 12 hini)
Malitro 0,31 / Mapainti 0,66
-
Mipimo ya vinthu vomwe ni vamadzilini
-
Homeri (Kori ibodzi / Maefa 10)
Malitro 220
-
Efa (Maseya yatatu / Maomeri 10)
Malitro 22
-
Seya (Maomeri 31 ⁄ 3)
Malitro 7,33
-
Omeri (Makabu 14 ⁄ 5)
Malitro 2,2 / Makwati 2
-
Kabu
Malitro 1,22 / Makwati 1,11
-
Kwati
Malitro 1,08
-
Vopimira nsenga
-
Ntsanga itali (Makovado 6 yataliyatali)
Mametro 3,11
-
Ntsanga (Makovado 6)
Mametro 2,67
-
Fatomu
Mametro 1,8
-
Kovado ibodzi (kupima maulendo 7 kumanja)
51,8 cm
-
Kovado (kupima kawiri kumanja / Kupima kumanja mfupimfupi maulendo 6)
44,5 cm
-
Kovado ifupi
38 cm
-
Shitadiyo ibodzi ya Chiroma
1 ⁄ 8 ya mailo ya Chiroma=1,85 m
-
1 Shitadiyo ibodzi ya Chiroma (1 ⁄ 4 ya mailo ya Chiroma)
Mametro 1,85
-
2 Kupima kumanja chamfupimfupi mwake (Vala 4 vophatana)
7,4 cm
-
3 Sipani (Kupima katatu kumanja)
22,2 cm