DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16 17 18 19 20 21 22 Buku la 1 Mafumu Machaputala 1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16 17 18 19 20 21 22 Mitu 1 Davide ndi Abisagi (1-4) Adoniya ankafuna kukhala mfumu (5-10) Zimene anachita Natani ndi Bati-seba (11-27) Davide analamula kuti Solomo adzozedwe kukhala mfumu (28-40) Adoniya anathawira kuguwa la nsembe (41-53) 2 Davide analangiza Solomo (1-9) Davide anamwalira; Solomo anakhala mfumu (10-12) Zimene Adoniya anachita zinamuphetsa (13-25) Abiyatara anathamangitsidwa; Yowabu anaphedwa (26-35) Simeyi anaphedwa (36-46) 3 Solomo anakwatira mwana wa Farao (1-3) Yehova anaonekera kwa Solomo mʼmaloto (4-15) Solomo anapempha nzeru (7-9) Solomo anaweruza azimayi awiri (16-28) 4 Ulamuliro wa Solomo (1-19) Zinthu zinkayenda bwino mu ulamuliro wa Solomo (20-28) Aliyense anali wotetezeka pansi pa mtengo wake wa mpesa ndi wa mkuyu (25) Nzeru za Solomo ndi miyambi yake (29-34) 5 Mfumu Hiramu anapereka zipangizo zomangira (1-12) Antchito yokakamiza a Solomo (13-18) 6 Solomo anamanga kachisi (1-38) Chipinda chamkati (19-22) Akerubi (23-28) Zogoba, zitseko, bwalo lamkati (29-36) Anamanga kachisi zaka pafupifupi 7 (37, 38) 7 Nyumba yachifumu ya Solomo (1-12) Hiramu waluso anathandiza Solomo (13-47) Zipilala ziwiri zakopa (15-22) Thanki yosungira madzi (23-26) Zotengera 10 zakopa (27-39) Anamaliza kupanga zinthu zagolide (48-51) 8 Anabweretsa Likasa mʼkachisi (1-13) Solomo analankhula ndi anthu (14-21) Pemphero la Solomo lotsegulira kachisi (22-53) Solomo anadalitsa anthu (54-61) Nsembe ndi chikondwerero chotsegulira kachisi (62-66) 9 Yehova anaonekeranso kwa Solomo (1-9) Mphatso zimene Solomo anapatsa Hiramu (10-14) Zinthu zimene Solomo anamanga (15-28) 10 Mfumukazi ya ku Sheba inakaona Solomo (1-13) Chuma chambiri cha Solomo (14-29) 11 Akazi a Solomo anapotoza mtima wake (1-13) Anthu amene ankalimbana ndi Solomo (14-25) Yerobowamu analonjezedwa mafuko (26-40) Solomo anamwalira; Rehobowamu anakhala mfumu (41-43) 12 Rehobowamu sanayankhe bwino anthu (1-15) Mafuko 10 anagalukira Solomo (16-19) Yerobowamu anakhala mfumu ya Isiraeli (20) Rehobowamu anamuletsa kuti asakamenyane ndi Aisiraeli (21-24) Yerobowamu anayamba kulambira mwana wa ngʼombe (25-33) 13 Ulosi wonena za guwa la ku Beteli (1-10) Guwa linagumuka (5) Munthu wa Mulungu sanamvere (11-34) 14 Ulosi wa Ahiya wotsutsa Yerobowamu (1-20) Rehobowamu anayamba kulamulira ku Yuda (21-31) Sisaki anaukira Yerusalemu (25, 26) 15 Abiyamu, mfumu ya Yuda (1-8) Asa, mfumu ya Yuda (9-24) Nadabu, mfumu ya Isiraeli (25-32) Basa, mfumu ya Isiraeli (33, 34) 16 Yehova anaweruza Basa (1-7) Ela, mfumu ya Isiraeli (8-14) Zimiri, mfumu ya Isiraeli (15-20) Omuri, mfumu ya Isiraeli (21-28) Ahabu, mfumu ya Isiraeli (29-33) Hiyeli anamanganso Yeriko (34) 17 Mneneri Eliya analosera chilala (1) Akhwangwala ankabweretsera Eliya chakudya (2-7) Eliya anapita kwa mkazi wamasiye wa ku Zarefati (8-16) Mwana wa mkazi wamasiye anamwalira nʼkuukitsidwa (17-24) 18 Eliya anakumana ndi Obadiya ndi Ahabu (1-18) Eliya ndi aneneri a Baala paphiri la Karimeli (19-40) ‘Mukayikakayika mpaka liti?’ (21) Chilala cha zaka zitatu ndi hafu chinatha (41-46) 19 Eliya anathawa Yezebeli (1-8) Yehova anaonekera kwa Eliya ku Horebe (9-14) Eliya anadzoza Hazaeli, Yehu ndi Elisa (15-18) Elisa anadzozedwa kuti alowe mʼmalo mwa Eliya (19-21) 20 Asiriya anamenyana ndi Ahabu (1-12) Ahabu anagonjetsa Asiriya (13-34) Ulosi wotsutsana ndi Ahabu (35-43) 21 Ahabu anasirira munda wa Naboti (1-4) Yezebeli anakonza zoti Naboti aphedwe (5-16) Uthenga wa Eliya wotsutsa Ahabu (17-26) Ahabu anadzichepetsa (27-29) 22 Yehosafati anachita mgwirizano ndi Ahabu (1-12) Mikaya analosera kuti Ahabu agonjetsedwa (13-28) Mzimu wabodza unapusitsa Ahabu (21, 22) Ahabu anaphedwa ku Ramoti-giliyadi (29-40) Yehosafati anakhala mfumu ya Yuda (41-50) Ahaziya mfumu ya Isiraeli (51-53) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena 1 Mafumu—Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) 1 Mafumu—Zimene Zili Mʼbukuli Chinenero Chamanja cha ku Malawi 1 Mafumu—Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt 1 Kings 586-587