DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 5 Kalata Yoyamba ya Petulo Machaputala 1 2 3 4 5 Mitu 1 Moni (1, 2) Kubadwanso mwatsopano nʼkukhala ndi chiyembekezo chodalirika (3-12) Mukhale oyera monga ana omvera (13-25) 2 Muzilakalaka Mawu a Mulungu (1-3) Miyala yamoyo ikumangidwa nʼkukhala nyumba yauzimu (4-10) Muzikhala ngati alendo mʼdzikoli (11, 12) Muzigonjera anthu oyenera kuwagonjera (13-25) Khristu ndi chitsanzo chathu (21) 3 Akazi komanso amuna apabanja (1-7) Muzimverana chisoni; muziyesetsa kumakhala mwamtendere (8-12) Kuvutika chifukwa chochita zinthu mwachilungamo (13-22) Muzikhala okonzeka kufotokoza za chiyembekezo chanu (15) Ubatizo komanso chikumbumtima chabwino (21) 4 Muzichita zimene Mulungu amafuna, ngati mmene Khristu ankachitira (1-6) Mapeto a zinthu zonse ayandikira (7-11) Kuvutika chifukwa chokhala Mkhristu (12-19) 5 Wetani gulu la nkhosa za Mulungu (1-4) Mukhale odzichepetsa komanso atcheru (5-11) Muzitula nkhawa zanu zonse kwa Mulungu (7) Mdyerekezi ali ngati mkango wobangula (8) Mawu omaliza (12-14) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena 1 Petulo—Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) 1 Petulo—Zimene Zili Mʼbukuli Chinenero Chamanja cha ku Malawi 1 Petulo—Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt 1 Peter 2051