DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 5 6 7 8 9 Buku la Amosi Machaputala 1 2 3 4 5 6 7 8 9 Mitu 1 Amosi analandira uthenga wochokera kwa Yehova (1, 2) Ziweruzo chifukwa chogalukira mobwerezabwereza (3-15) Siriya (3-5), Filisitiya (6-8), Turo (9, 10), Edomu (11, 12), Amoni (13-15) 2 Ziweruzo chifukwa chogalukira mobwerezabwereza (1-16) Mowabu (1-3), Yuda (4, 5), Isiraeli (6-16) 3 Kulengeza uthenga wachiweruzo wa Mulungu (1-8) Mulungu anaulula chinsinsi chake (7) Uthenga wotsutsana ndi Samariya (9-15) 4 Uthenga wotsutsana ndi ngʼombe za ku Basana (1-3) Yehova ananyoza kulambira kwabodza kwa Aisiraeli (4, 5) Aisiraeli anakana kubwerera kwa Mulungu (6-13) “Konzekera kukumana ndi Mulungu wako” (12) ‘Mulungu amafotokozera munthu zimene akuganiza’ (13) 5 Isiraeli anali ngati namwali wakugwa (1-3) Funafunani Mulungu kuti mukhale ndi moyo (4-17) Muzidana ndi zoipa nʼkumakonda zabwino (15) Tsiku la Yehova ndi tsiku lamdima (18-27) Nsembe za Aisiraeli zinakanidwa (22) 6 Tsoka kwa anthu okhala mosatekeseka (1-14) Mabedi aminyanga ya njovu; makapu a vinyo (4, 6) 7 Masomphenya osonyeza kuti mapeto a Aisiraeli ali pafupi (1-9) Dzombe (1-3), moto (4-6), chingwe choyezera (7-9) Amosi anauzidwa kuti asiye kunenera (10-17) 8 Masomphenya a dengu la zipatso zamʼchilimwe (1-3) Anthu opondereza anzawo anadzudzulidwa (4-14) Njala yauzimu (11) 9 Nʼzosatheka kuthawa chiweruzo cha Mulungu (1-10) Nyumba ya Davide inadzutsidwanso (11-15) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Amosi—Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) Amosi—Zimene Zili Mʼbukuli Chinenero Chamanja cha ku Malawi Amosi—Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt Amos 1576-1577