Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yopita kwa Aroma

Machaputala

1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16

Mitu

  • 1

    • Mawu oyamba (1-7)

    • Paulo ankafunitsitsa kupita ku Roma (8-15)

    • Wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha chikhulupiriro (16, 17)

    • Anthu alibe chifukwa chosakhulupirira kuti kuli Mulungu (18-32)

      • Makhalidwe a Mulungu amaoneka mu zinthu zimene analenga (20)

  • 2

    • Chiweruzo cha Mulungu kwa Ayuda ndi Agiriki (1-16)

      • Mmene chikumbumtima chimagwirira ntchito (14, 15)

    • Ayuda ndiponso Chilamulo (17-24)

    • Mdulidwe wa mumtima (25-29)

  • 3

    • ‘Mulungu amanena zoona’ (1-8)

    • Ayuda ndi Agiriki omwe ndi ochimwa (9-20)

    • Kukhala wolungama chifukwa cha chikhulupiriro (21-31)

      • Anthu onse amalephera kusonyeza bwinobwino ulemerero wa Mulungu (23)

  • 4

    • Abulahamu anaonedwa kuti ndi wolungama chifukwa cha chikhulupiriro (1-12)

      • Abulahamu, bambo wa anthu a chikhulupiriro (11)

    • Analandira lonjezo chifukwa cha chikhulupiriro (13-25)

  • 5

    • Kugwirizananso ndi Mulungu kudzera mwa Khristu (1-11)

    • Timafa chifukwa cha Adamu, timakhala ndi moyo chifukwa cha Khristu (12-21)

      • Uchimo ndi imfa zinafalikira kwa anthu onse (12)

      • Kuchita chinthu chimodzi cholungama (18)

  • 6

    • Moyo watsopano kudzera mu ubatizo wogwirizana ndi Khristu (1-11)

    • Musalole kuti uchimo uzilamulira matupi anu (12-14)

    • Kuchoka ku ukapolo wauchimo nʼkukhala akapolo a Mulungu (15-23)

      • Malipiro a uchimo ndi imfa; mphatso ya Mulungu ndi moyo (23)

  • 7

    • Fanizo losonyeza mmene munthu amamasukira ku Chilamulo (1-6)

    • Chilamulo chinathandiza kuti uchimo uonekere (7-12)

    • Kulimbana ndi uchimo (13-25)

  • 8

    • Mzimu umabweretsa moyo ndi ufulu (1-11)

    • Mzimu umachitira umboni (12-17)

    • Chilengedwe chikudikira ufulu wa ana a Mulungu (18-25)

    • ‘Mzimu umachonderera mʼmalo mwathu’ (26, 27)

    • Mulungu anawasankhiratu (28-30)

    • Tikugonjetsa zinthu zonse chifukwa cha chikondi cha Mulungu (31-39)

  • 9

    • Paulo ankamvera chisoni Aisiraeli (1-5)

    • Mbadwa zenizeni za Abulahamu (6-13)

    • Palibe angatsutse zimene Mulungu wasankha (14-26)

      • Ziwiya za mkwiyo ndiponso ziwiya za chifundo (22, 23)

    • Anthu ochepa okha ndi amene adzapulumuke (27-29)

    • Aisiraeli anapunthwa (30-33)

  • 10

    • Mmene tingakhalire olungama pamaso pa Mulungu (1-15)

      • Kulengeza poyera (10)

      • Oitana pa dzina la Yehova adzapulumuka (13)

      • Mapazi a anthu olalikira ndi okongola (15)

    • Ena anakana uthenga wabwino (16-21)

  • 11

    • Si Aisiraeli onse amene anakanidwa (1-16)

    • Fanizo la mtengo wa maolivi (17-32)

    • Nzeru za Yehova nʼzozama (33-36)

  • 12

    • Mupereke matupi anu ngati nsembe ya moyo (1, 2)

    • Thupi limodzi koma mphatso zosiyanasiyana (3-8)

    • Malangizo okhudza moyo wa Chikhristu (9-21)

  • 13

    • Kugonjera olamulira (1-7)

      • Kukhoma misonkho (6, 7)

    • Chikondi chimakwaniritsa Chilamulo (8-10)

    • Tizichita zinthu ngati masana (11-14)

  • 14

    • Tisamaweruze ena (1-12)

    • Tisamakhumudwitse ena (13-18)

    • Tiziyesetsa kukhala mwamtendere komanso mogwirizana (19-23)

  • 15

    • Tizilandirana ngati mmene Khristu anatilandirira (1-13)

    • Paulo, mtumiki wa anthu a mitundu ina (14-21)

    • Maulendo amene Paulo ankafuna kuyenda (22-33)

  • 16

    • Paulo anauza anthu za Febe yemwe ankatumikira mumpingo (1, 2)

    • Moni wopita kwa Akhristu a ku Roma (3-16)

    • Anachenjeza za kugawikana (17-20)

    • Moni wochokera kwa anzake a Paulo (21-24)

    • Chinsinsi chopatulika tsopano chadziwika (25-27)