DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16 17 18 19 20 21 22 23 24 25 26 27 28 29 30 31 32 33 34 Buku la Deuteronomo Machaputala 1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16 17 18 19 20 21 22 23 24 25 26 27 28 29 30 31 32 33 34 Mitu 1 Kuchoka paphiri la Horebe (1-8) Anasankha atsogoleri komanso oweruza (9-18) Anthu sanamvere ku Kadesi-barinea (19-46) Aisiraeli anakana kulowa mʼdziko (26-33) Analephera kugonjetsa Akanani (41-46) 2 Anayenda mʼchipululu kwa zaka 38 (1-23) Anagonjetsa Mfumu Sihoni ya ku Hesiboni (24-37) 3 Anagonjetsa Mfumu Ogi ya ku Basana (1-7) Malire a dziko kumʼmawa kwa mtsinje wa Yorodano (8-20) Yoswa anauzidwa kuti asachite mantha (21, 22) Mose sadzalowa mʼdziko (23-29) 4 Anawalimbikitsa kuti akhale omvera (1-14) Musaiwale zimene Mulungu anachita (9) Yehova amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha (15-31) Palibe Mulungu wina kupatulapo Yehova (32-40) Mizinda yothawirako kumʼmawa kwa Yorodano (41-43) Anawapatsa Chilamulo (44-49) 5 Yehova anachita pangano ku Horebe (1-5) Anabwereza kuwauza Malamulo Khumi (6-22) Anthu anachita mantha paphiri la Sinai (23-33) 6 Muzikonda Yehova ndi mtima wanu wonse (1-9) “Tamverani Aisiraeli inu” (4) Makolo aziphunzitsa ana (6, 7) Musaiwale Yehova (10-15) Musamamuyese Yehova (16-19) Mudzafotokozere mʼbadwo wotsatira (20-25) 7 Mitundu 7 yoyenera kuwonongedwa (1-6) Chifukwa chimene anasankhira Aisiraeli (7-11) Kumvera kumabweretsa madalitso (12-26) 8 Anawauzanso madalitso amene Yehova adzawapatse (1-9) “Munthu sakhala ndi moyo ndi chakudya chokha” (3) Musaiwale Yehova (10-20) 9 Chifukwa chake Aisiraeli anapatsidwa dziko (1-6) Aisiraeli anakwiyitsa Yehova maulendo 4 (7-29) Mwana wa ngʼombe wagolide (7-14) Mose anachonderera Yehova (15-21, 25-29) Anamukwiyitsanso maulendo ena atatu (22) 10 Anapanganso miyala yosema iwiri (1-11) Zimene Yehova amafuna (12-22) Muziopa komanso kukonda Yehova (12) 11 Mwaona mphamvu za Yehova (1-7) Dziko Lolonjezedwa (8-12) Madalitso amene adzapeze chifukwa chomvera (13-17) Muzisunga mawu a Mulungu mʼmitima yanu (18-25) “Dalitso ndi temberero” (26-32) 12 Muzilambira pamalo amene Mulungu anasankha (1-14) Analoledwa kudya nyama koma osati magazi (15-28) Musagwidwe mʼmisampha ya milungu ina (29-32) 13 Zoyenera kuchita ndi ampatuko (1-18) 14 Zinthu zosayenera kuchita polira maliro (1, 2) Zakudya zodetsedwa komanso zosadetsedwa (3-21) Chakhumi choperekedwa kwa Yehova (22-29) 15 Ankakhululukira angongole chaka cha 7 chilichonse (1-6) Kuthandiza osauka (7-11) Akapolo ankamasulidwa chaka cha 7 chilichonse (12-18) Kuboola khutu la kapolo (16, 17) Nyama zoyamba kubadwa zinali zopatulika (19-23) 16 Pasika; Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa (1-8) Chikondwerero cha Masabata (9-12) Chikondwerero cha Misasa (13-17) Kusankha oweruza (18-20) Zinthu zosayenera kuzilambira (21, 22) 17 Nsembe zizikhala zopanda chilema (1) Zoyenera kuchita ndi ampatuko (2-7) Milandu yovuta kuweruza (8-13) Malangizo oti mafumu azidzatsatira (14-20) Mfumu izikopera buku la Chilamulo (18) 18 Zimene ansembe ndi Alevi ankayenera kulandira (1-8) Anawaletsa kuchita zamizimu (9-14) Mneneri ngati Mose (15-19) Mmene tingadziwire aneneri abodza (20-22) 19 Mlandu wa magazi komanso mizinda yothawirako (1-13) Zizindikiro za malire sizinkafunika kusunthidwa (14) Anthu operekera umboni mukhoti (15-21) Pankafunika mboni ziwiri kapena zitatu (15) 20 Malamulo okhudza nkhondo (1-20) Anthu amene samayenera kupita kunkhondo (5-9) 21 Ngati wopha munthu sakudziwika (1-9) Kukwatira akazi ogwidwa kunkhondo (10-14) Ufulu wa mwana woyamba kubadwa (15-17) Mwana wosamvera (18-21) Munthu wopachikidwa pamtengo ndi wotembereredwa (22, 23) 22 Kulemekeza ziweto za anthu ena (1-4) Kuvala zovala zachimuna kapena zachikazi (5) Kuchitira chifundo ziweto (6, 7) Kampanda kapadenga la nyumba (8) Zinthu zosayenera kuphatikizidwa (9-11) Ulusi wa mʼmphepete mwa zovala (12) Malamulo a milandu yokhudza kugonana (13-30) 23 Anthu osayenera kulowa mumpingo wa Mulungu (1-8) Ukhondo mumsasa (9-14) Kapolo amene wathawa kwa mbuye wake (15, 16) Uhule unaletsedwa (17, 18) Chiwongoladzanja komanso malonjezo (19-23) Zimene anthu ongodutsa ankaloledwa kudya (24, 25) 24 Ukwati komanso kutha kwa ukwati (1-5) Kulemekeza moyo (6-9) Kuganizira osauka (10-18) Malamulo okhudza kukunkha (19-22) 25 Malamulo okhudza kukwapula munthu (1-3) Ngʼombe imene ikupuntha mbewu musamaimange pakamwa (4) Ukwati wapachilamu (5-10) Kugwira malo osayenera pandewu (11, 12) Muyezo woyenera woyezera kulemera komanso kuchuluka kwa zinthu (13-16) Aamaleki ayenera kuwonongedwa (17-19) 26 Kupereka zipatso zoyambirira (1-11) Chakhumi chachiwiri (12-15) Aisiraeli anali chuma chapadera kwa Yehova (16-19) 27 Akalembe Chilamulo pamiyala (1-10) Paphiri la Ebala ndi paphiri la Gerizimu (11-14) Anatchulanso matemberero (15-26) 28 Madalitso chifukwa chomvera (1-14) Matemberero chifukwa chosamvera (15-68) 29 Anachita pangano ndi Aisiraeli ku Mowabu (1-13) Anawachenjeza kuti apewe kusamvera (14-29) Zinthu zobisika, zinthu zoululidwa (29) 30 Kubwerera kwa Yehova (1-10) Malamulo a Yehova si ovuta kwambiri (11-14) Kusankha moyo kapena imfa (15-20) 31 Mose anali atatsala pangʼono kumwalira (1-8) Kuwerenga Chilamulo pamaso pa anthu (9-13) Yoswa anamuika kuti akhale mtsogoleri (14, 15) Ananeneratu kuti Aisiraeli adzapandukira Mulungu (16-30) Nyimbo yoti aphunzitse Aisiraeli (19, 22, 30) 32 Nyimbo ya Mose (1-47) Yehova ndi Thanthwe (4) Aisiraeli anaiwala Thanthwe lawo (18) “Kubwezera ndi kwanga” (35) “Inu anthu a mitundu ina, sangalalani limodzi ndi anthu ake” (43) Mose akafera mʼphiri la Nebo (48-52) 33 Mose anadalitsa mafuko (1-29) Manja a Yehova “omwe adzakhalapo mpaka kalekale” (27) 34 Yehova anaonetsa Mose dziko (1-4) Imfa ya Mose (5-12) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Deuteronomo—Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) Deuteronomo—Zimene Zili Mʼbukuli Chinenero Chamanja cha ku Malawi Deuteronomo—Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt Deuteronomy 334-336