Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Maliro

Machaputala

1 2 3 4 5

Mitu

  • 1

    • Yerusalemu anayerekezeredwa ndi mkazi wamasiye

      • Yerusalemu anatsala yekhayekha wopanda munthu (1)

      • Machimo aakulu a Ziyoni (8, 9)

      • Ziyoni anakanidwa ndi Mulungu (12-15)

      • Palibe aliyense amene akutonthoza Ziyoni (17)

  • 2

    • Yehova anakwiyira Yerusalemu

      • Sanamve chisoni (2)

      • Yehova anakhala ngati mdani wake (5)

      • Kulirira Ziyoni (11-13)

      • Anthu odutsa mumsewu ananyoza mzinda umene poyamba unali wokongola (15)

      • Adani anasangalala chifukwa cha kuwonongedwa kwa Ziyonil (17)

  • 3

    • Yeremiya anasonyeza mmene akumvera komanso zimene ankayembekezera

      • “Ndidzakhala ndi mtima wodikira” (21)

      • Chifundo cha Mulungu chimakhala chatsopano mʼmawa uliwonse (22, 23)

      • Mulungu ndi wabwino kwa anthu amene akumuyembekezera (25)

      • Ndi bwino kuti munthu akumane ndi mavuto ali wamngʼono (27)

      • Mulungu anadzitchinga ndi mtambo (43, 44)

  • 4

    • Mavuto oopsa amene Yerusalemu anakumana nawo atazunguliridwa ndi adani

      • Kusowa kwa chakudya (4, 5, 9)

      • Azimayi anaphika ana awo (10)

      • Yehova anakhuthula mkwiyo wake (11)

  • 5

    • Pemphero la anthu lopempha kuti zinthu zibwerere mwakale

      • ‘Kumbukirani zimene zatichitikira’ (1)

      • ‘Tsoka kwa ife chifukwa tachimwa’ (16)

      • ‘Inu Yehova, tibwezereni kwa inu’ (21)

      • “Bwezeretsani zinthu zonse” (21)