DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 5 6 7 Buku la Mika Machaputala 1 2 3 4 5 6 7 Mitu 1 Chiweruzo cha Samariya ndi Yuda (1-16) Machimo ndi kugalukira zinabweretsa mavuto (5) 2 Tsoka kwa opondereza anzawo (1-11) Aisiraeli anagwirizanitsidwa (12, 13) Mʼdziko mudzadzaza phokoso la anthu (12) 3 Atsogoleri ndi aneneri anadzudzulidwa (1-12) Mika anapatsidwa mphamvu ndi mzimu wa Yehova (8) Ansembe ankaphunzitsa kuti apeze ndalama (11) Yerusalemu adzakhala bwinja (12) 4 Phiri la Yehova lidzakwezedwa (1-5) Kusula malupanga kuti akhale makasu a pulawo (3) ‘Ife tidzayenda mʼdzina la Yehova’ (5) Ziyoni adzakhalanso wamphamvu (6-13) 5 Wolamulira amene adzakhale wamphamvu padziko lonse (1-6) Wolamulira adzachokera ku Betelehemu (2) Anthu otsala adzakhala ngati mame komanso mkango (7-9) Dziko lidzayeretsedwa (10-15) 6 Mulungu anaimba mlandu Aisiraeli (1-5) Yehova akufuna kuti uzichita chiyani? (6-8) Chilungamo, kukhulupirika, kudzichepetsa (8) Aisiraeli analakwa nʼkulangidwa (9-16) 7 Makhalidwe oipa a Aisiraeli (1-6) Adani a munthu adzakhala anthu a mʼbanja lake (6) “Ine ndidzayembekezera Yehova” (7) Anthu a Mulungu zinthu zidzawayendera bwino (8-13) Mika anapemphera komanso kutamanda Mulungu (14-20) Yehova anayankha (15-17) ‘Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi Yehova?’ (18) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Mika—Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) Mika—Zimene Zili Mʼbukuli Chinenero Chamanja cha ku Malawi Mika—Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt Micah 1595-1596