Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Nehemiya

Machaputala

1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13

Mitu

  • 1

    • Uthenga wochokera ku Yerusalemu (1-3)

    • Pemphero la Nehemiya (4-11)

  • 2

    • Nehemiya anatumizidwa ku Yerusalemu (1-10)

    • Nehemiya anayendera mpanda (11-20)

  • 3

    • Ntchito yokonza mpanda (1-32)

  • 4

    • Ntchito inkayenda bwino ngakhale kuti ankatsutsidwa (1-14)

    • Anthu ankamanga atanyamula zida (15-23)

  • 5

    • Nehemiya analetsa kudyerana masuku pamutu (1-13)

    • Nehemiya sanali wodzikonda (14-19)

  • 6

    • Anthu ankatsutsabe ntchito yomanga (1-14)

    • Mpanda unamalizidwa mʼmasiku 52 (15-19)

  • 7

    • Mageti a mzinda ndiponso alonda apageti (1-4)

    • Anthu amene anabwera ku ukapolo (5-69)

      • Atumiki apakachisi (46-56)

      • Ana a atumiki a Solomo (57-60)

    • Zopereka zothandiza pa ntchito (70-73)

  • 8

    • Anawerengera anthu Chilamulo ndiponso kuwafotokozera (1-12)

    • Anachita Chikondwerero cha Misasa (13-18)

  • 9

    • Anthu analapa machimo awo (1-38)

      • Yehova ndi Mulungu wokhululuka (17)

  • 10

    • Anthu anavomereza kuti azitsatira Chilamulo (1-39)

      • “Sitidzanyalanyaza nyumba ya Mulungu wathu” (39)

  • 11

    • Anthu anayambiranso kukhala ku Yerusalemu (1-36)

  • 12

    • Ansembe ndiponso Alevi (1-26)

    • Mwambo wotsegulira mpanda (27-43)

    • Kuthandiza ntchito zapakachisi (44-47)

  • 13

    • Zinthu zinanso zimene Nehemiya anasintha (1-31)

      • Kupereka chakhumi (10-13)

      • Osaipitsa tsiku la Sabata (15-22)

      • Anawaletsa kukwatirana ndi anthu a mitundu ina (23-28)