DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 5 Kalata ya Yakobo Machaputala 1 2 3 4 5 Mitu 1 Moni (1) Kupirira kumachititsa kuti tikhale osangalala (2-15) Chikhulupiriro chimakhala cholimba tikamayesedwa (3) Tizipempha ndi chikhulupiriro (5-8) Chilakolako chimabweretsa uchimo ndi imfa (14, 15) Mphatso iliyonse yabwino imachokera kumwamba (16-18) Kumva ndi kuchita zimene mawu akunena (19-25) Munthu amene akudziyangʼanira pagalasi (23, 24) Kulambira koyera komanso kosadetsedwa (26, 27) 2 Kuchita zokondera ndi tchimo (1-13) Chikondi ndi lamulo lachifumu (8) Chikhulupiriro chopanda ntchito zake ndi chakufa (14-26) Ziwanda zimakhulupirira ndipo zimanjenjemera (19) Abulahamu ankadziwika kuti ndi mnzake wa Yehova (23) 3 Kuweta lilime (1-12) Pasakhale aphunzitsi ambiri (1) Nzeru yochokera kumwamba (13-18) 4 Musachite ubwenzi ndi dziko (1-12) Tsutsani Mdyerekezi (7) Yandikirani Mulungu (8) Anawachenjeza kuti apewe kunyada (13-17) “Yehova akalola” (15) 5 Anachenjeza anthu achuma (1-6) Mulungu amadalitsa anthu amene amayembekezera moleza mtima (7-11) Mukati “ayi,” azikhaladi ayi (12) Pemphero lachikhulupiriro limagwira ntchito (13-18) Kuthandiza munthu wochimwa kuti abwerere (19, 20) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Yakobo—Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) Yakobo—Zimene Zili Mʼbukuli Chinenero Chamanja cha ku Malawi Yakobo—Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt James 2044-2045