A7-E
Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu MʼGalileya (Gawo 3) Komanso ku Yudeya
NTHAWI |
MALO |
ZIMENE ZINACHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
32, pambuyo pa Pasika |
Nyanja ya Galileya; Betsaida |
Ali mʼngalawa popita ku Betsaida, Yesu anachenjeza za chofufumitsa cha Afarisi; anachiritsa wosaona |
||||
Ku Kaisareya wa Filipi |
Makiyi a Ufumu; aneneratu za imfa yake ndi kuukitsidwa |
|||||
Paphiri la Herimoni |
Anasandulika; Yehova analankhula |
|||||
Ku Kaisareya wa Filipi |
Anachiritsa mnyamata wogwidwa ndi ziwanda |
|||||
Galileya |
Aneneratunso za imfa yake |
|||||
Kaperenao |
Anapereka ndalama ya msonkho |
|||||
Wamkulu kwambiri mu Ufumu; fanizo la nkhosa yosochera ndi la kapolo wosakhululuka |
||||||
Galileya-Samariya |
Akupita ku Yerusalemu, anauza ophunzira kuika patsogolo Ufumu |
Utumiki Womaliza Umene Yesu Anachita ku Yudeya
NTHAWI |
MALO |
ZIMENE ZINACHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
32, Chikondwerero cha Misasa (kapena kuti, Mahema) |
Yerusalemu |
Anaphunzitsa pa Chikondwerero; asilikali anatumidwa kukamanga Yesu |
||||
Anati “Ine ndine kuwala kwa dziko”; anachiritsa munthu wosaona |
||||||
Mwina ku Yudeya |
Anatumiza ophunzira 70 kukalalikira |
|||||
Yudeya; Betaniya |
Fanizo la Msamariya wachifundo; anapita kwa Mariya ndi Marita |
|||||
Mwina ku Yudeya |
Pemphero lachitsanzo; fanizo lokhudza kulimbikira kupemphera |
|||||
Anatulutsa ziwanda; anaperekanso chizindikiro cha Yona |
||||||
Anadya ndi Mfarisi; anadzudzula chinyengo cha Afarisi |
||||||
Mafanizo: wolemera wopanda nzeru komanso mtumiki wokhulupirika |
||||||
Anachiritsa mzimayi wopindika msana pa Sabata; fanizo la kanjere ka mpiru ndi la zofufumitsa |
||||||
32, Kupereka Kachisi |
Yerusalemu |
Fanizo la mʼbusa wabwino; Ayuda ankafuna kumugenda; anapita ku Betaniya wakutsidya la Yorodano |