A7-F
Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Utumiki Womaliza Umene Yesu Anachita Kumʼmawa kwa Yorodano
NTHAWI |
MALO |
ZIMENE ZINACHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
32, pambuyo pa Chikondwerero Chopereka Kachisi kwa Mulungu |
Betaniya wakutsidya kwa Yorodano |
Anapita kumene Yohane ankabatizira; ambiri anakhulupirira Yesu |
||||
Pereya |
Anaphunzitsa mʼmizinda ndi mʼmidzi, akulowera ku Yerusalemu |
|||||
Anawauza kuti alowe pakhomo lalingʼono; anadandaulira Yerusalemu |
||||||
Mwina ku Pereya |
Anaphunzitsa za kudzichepetsa; mafanizo: malo olemekezeka komanso alendo amene sanabwere kuphwando |
|||||
Udindo wokhala wophunzira |
||||||
Mafanizo: nkhosa yosowa, ndalama yotaika, mwana wolowerera |
||||||
Mafanizo: mtumiki wosalungama, munthu wolemera ndi Lazaro |
||||||
Anaphunzitsa za kukhumudwitsana, kukhululukirana ndi chikhulupiriro |
||||||
Betaniya |
Lazaro anamwalira ndi kuukitsidwa |
|||||
Yerusalemu; Efuraimu |
Chiwembu chopha Yesu; anachokako |
|||||
Samariya; Galileya |
Anachiritsa akhate 10; anaphunzitsa za kubwera kwa Ufumu wa Mulungu |
|||||
Samariya kapena Galileya |
Mafanizo: mkazi wamasiye wakhama, Mfarisi ndi wokhometsa msonkho |
|||||
Pereya |
Anaphunzitsa zokhudza ukwati |
|||||
Anadalitsa ana |
||||||
Funso la munthu wolemera; fanizo la antchito amʼmunda wa mpesa ndi malipiro ofanana |
||||||
Mwina ku Pereya |
Kachitatu ananeneratu za imfa yake |
|||||
Yakobo ndi Yohane anapempha malo mu Ufumu |
||||||
Yeriko |
Podutsa, anachiritsa amuna awiri osaona; anapita kwa Zakeyu; fanizo la ndalama zokwana ma mina 10 |