A7-C
Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu MʼGalileya (Gawo 1)
NTHAWI |
MALO |
ZIMENE ZINACHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
30 |
Galileya |
Choyamba Yesu analengeza kuti “Ufumu wakumwamba wayandikira” |
||||
Kana; Nazareti; Kaperenao |
Anachiritsa mnyamata; anawerenga mpukutu wa Yesaya; ku Kaperenao |
|||||
Nyanja ya Galileya, pafupi ndi Kaperenao |
Anaitana ophunzira 4: Simoni ndi Andireya, Yakobo ndi Yohane |
|||||
Kaperenao |
Kuchiritsa apongozi a Simoni ndi ena |
|||||
Galileya |
Ulendo woyamba ndi ophunzira 4 |
|||||
Kuchiritsa wakhate; anthu anapita kwa Yesu |
||||||
Kaperenao |
Anachiritsa munthu wakufa ziwalo |
|||||
Anaitana Mateyu; anadya ndi okhometsa msonkho; anamufunsa za kusala |
||||||
Yudeya |
Analalikira mʼmasunagoge |
|||||
31, Pasika |
Yerusalemu |
Anachiritsa mwamuna wina ku Betizata; Ayuda ankafuna kumupha |
||||
Kubwerera kuchokera ku Yerusalemu (?) |
Ankabudula ngala za tirigu pa Sabata; Yesu ndi “Mbuye wa Sabata” |
|||||
Galileya; Nyanja ya Galileya |
Anachiritsa wolumala pa Sabata; anthu anamutsatira; anachiritsa ena |
|||||
Phiri la ku Kaperenao |
Anasankha atumwi 12 |
|||||
Pafupi ndi Kaperenao |
Ulaliki wapaphiri |
|||||
Kaperenao |
Anachiritsa wantchito wa msilikali |
|||||
Naini |
Anaukitsa mwana wa mkazi wamasiye |
|||||
Tiberiyo; Galileya (Naini kapena pafupi) |
Yohane anatumiza ophunzira ake kwa Yesu; choonadi chinaululidwa kwa ana aangʼono; goli losavuta kunyamula |
|||||
Galileya (Naini kapena pafupi) |
Mzimayi wochimwa anathira mafuta pamapazi ake; fanizo la angongole |
|||||
Galileya |
Ulendo wachiwiri wokalalikira |
|||||
Anatulutsa ziwanda; tchimo losakhululukidwa |
||||||
Anapereka chizindikiro cha Yona |
||||||
Kunabwera mayi ndi azichimwene ake; anati abale ake ndi ophunzira ake |