Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

B14-A

Miyezo ya Zinthu Ndiponso Malonda

  • Miyezo ya Zinthu Zamadzi

  • Kori (Mitsuko 10 / Mahini 60)

    Malita 220 / Magaloni 58.1

  • Mtsuko (Mahini 6)

    Malita 22 / Magaloni 5.81

  • Hini (Malogi 12)

    Malita 3.67 / Mapainti 7.75

  • Logi (1⁄12 hini)

    Malita 0.31 / Mapainti 0.66

  • Miyezo ya Zinthu Zomwe Si Zamadzi

  • Homeri (Kori imodzi / Maefa 10)

    Malita 220

  • Efa (Maseya atatu / Maomeri 10)

    Malita 22

  • Seya (Maomeri 31⁄3)

    Malita 7.33

  • Omeri (Makabu 14⁄5)

    Malita 2.2 / Makwati 2

  • Kabu

    Malita 1.22 / Makwati 1.11

  • Kwati

    Malita 1.08

  • Miyezo Yoyezera Mtunda

  • Bango lalitali (Mikono 6 yaitali)

    Mamita 3.11 / Mafiti 10.2

  • Bango (Mikono 6)

    Mamita 2.67 / Mafiti 8.75

  • Fatomu

    Mamita 1.8 / Mafiti 6

  • Mkono umodzi (Zikhatho 7)

    Masentimita 51.8 / Mainchesi 20.4

  • Mkono (Masipani awiri / Zikhatho 6)

    Masentimita 44.5 / Mainchesi 17.5

  • Mkono waufupi

    Masentimita 38 / Mainchesi 15

  • Sitadiya imodzi ya Chiroma 1⁄8 ya mailo ya Chiroma

    = Mamita 185 / Mafiti 606.95

  1. 1 Mphipi imodzi ya chala (1⁄4 ya chikhatho)

    Masentimita 1.85 / Mainchesi 0.73

  2. 2 Chikhatho (Mphipi ya zala 4)

    Masentimita 7.4 / Mainchesi 2.9

  3. 3 Sipani (Zikhatho zitatu)

    Masentimita 22.2 / Mainchesi 8.75