B15
Kalendala ya Chiheberi
NISANI (ABIBU) March—April |
14 Pasika 15-21 Mkate Wopanda Zofufumitsa 16 Nsembe ya zipatso zoyamba kucha |
Yorodano ankasefukira chifukwa cha mvula ndi madzi osungunuka |
Balere |
IYARA (ZIVI) April—May |
14 Pasika Wochitika Nthawi Yake Itadutsa |
Nthawi ya chilimwe, kumwamba kopanda mitambo |
Tirigu |
SIVANI May—June |
6 Chikondwerero cha Masabata (Pentekosite) |
Kunja kunkatentha koma kunkakhala mpweya wabwino |
Tirigu, nkhuyu zoyambirira |
TAMUZI June—July |
Kutentha kunkawonjezereka, mame ankagwa ambiri |
Mphesa zoyambirira |
|
ABI July—August |
Kutentha kunkafika pachimake |
Zipatso zamʼchilimwe |
|
ELULI August—September |
Kutentha kunkapitirira |
Kanjedza, mphesa ndi nkhuyu |
|
TISHIRI (ETANIMU) September—October |
1 Tsiku loliza lipenga 10 Mwambo Wophimba Machimo 15-21 Chikondwerero cha Misasa 22 Msonkhano wapadera |
Chilimwe chikutha, mvula ikuyamba |
Kulima |
HESHIVANI (BULI) October—November |
Mvula yowaza— |
Maolivi |
|
KISILEVI November—December |
25 Chikondwerero cha Kupereka Kachisi wa Mulungu |
Mvula inkawonjezereka, madzi ankaundana mʼmapiri |
Nyengo yozizira ziweto zinkakhala mʼkhola |
TEBETI December—January |
Kunkazizira kwambiri, kunkagwa mvula, madzi ankaundana mʼmapiri |
Zomera zikukula |
|
SEBATI January—February |
Kuzizira kunkacheperako, mvula inkapitiriza kugwa |
Amondi ankachita maluwa |
|
ADARA February—March |
14, 15 Purimu |
Kunkachitika mabingu, kunkagwa mvula yamatalala |
Fulakesi |
VEADARA March |
Pa zaka 19 zilizonse, zaka 7 zinkakhala ndi mwezi wowonjezera |