October 2-8

YOBU 1-3

October 2-8
  • Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 21

  • Ndinkaganiza Ngati Ndili Ndi Chilichonse: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: N’chifukwa chiyani M’bale Birdwell ankaganiza kuti anali ndi chilichonse?

    Kodi kuganizira mfundo ya pa lemba la Mateyu 6:33 kunathandiza bwanji m’baleyu?

    Kodi mwaphunzirapo chiyani pa chitsanzo cha banja la a Birdwell?

  • Muzigwiritsa Ntchito Tsamba Loyamba la JW.ORG Mukakhala mu Utumiki”: (5 min.) Nkhani yokambirana.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 51

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero