CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova YAMBANI Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu [Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yobu.] Satana ankanena kuti Yobu ankatumikira komanso kukonda Yehova chifukwa cha dyera (Yob 1:8-11; w18.02 2:16-17) Satana amanena kuti ifenso sitikonda Yehova ndi mtima wonse (Yob 2:4, 5; w19.02 6:10) Yehova anapereka mwayi kwa tonsefe woti tizisonyeza kuti Satana ndi wabodza. (Miy 27:11) Tingasonyeze kuti timakonda kwambiri Yehova pochita zinthu zomusangalatsa kaya zinthu zili bwino pa moyo wathu kapena ayi. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova Chinenero Chamanja cha ku Malawi Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/202023332/univ/art/202023332_univ_sqr_xl.jpg mwb23.9 13