October 23-29 YOBU 8-10 YAMBANI October 23-29 Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero Mawu Oyamba (1 min.) CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana”: (10 min.) Mfundo Zothandiza: (10 min.) Yob 9:32—Kodi tizitani ngati tawerenga nkhani inayake m’Baibulo imene sitikuimvetsa? (w10 10/15 6-7 ¶19-20) Yankho Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina? Yankho Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 9:20-35 (th phunziro 11) KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 17) Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku ka Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo kambiranani naye mwachidule mfundo zimene zili pa mutu wakuti “Zimene Mungachite Kuti Muzipindula ndi Phunziro Lililonse.” (th phunziro 3) Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 16 mfundo 6 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 14) MOYO WATHU WACHIKHRISTU Nyimbo Na. 109 “Muzithandiza Anthu Osapembedza Kudziwa Mlengi Wawo”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo. Zofunika Pampingo: (5 min.) Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) bt “Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira” komanso mutu 1 ¶1-7 Mawu Omaliza (3 min.) Nyimbo Na. 64 ndi Pemphero Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena October 23-29 UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO Ndandanda ya Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya October 23-29, 2023 Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ndandanda ya Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya October 23-29, 2023 https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/202023339/univ/art/202023339_univ_sqr_xl.jpg mwb23.9 20